Petition Closed

Boma la Malawi likuyenera kukana mfundo yofuna kuyenga mafuta mu Nyanja ya Malawi. Kampani yakku UK yochedwa Surestream yinatumidwa kuti yifufuze mafuta pa Nyanjayi kopanda chilolezo cha a Malawi. Zikwi zikwi za a Malawi zimadallira nyanjayi pa phindu,chakudya ndi madzi akumwa. Enanso ambiri amasangalala ndi kukongora kwa nyanjayi. A Malawi akudziwa kuti kuyenga mafuta kutayambidwa pa nyanjayi,phindu lake lizapita kunja ndipo a Malawi osauka.

“POSTAL CODE” mutha kungoikapo manambala asanu ena aliwonse chifukwa simutha kutumiza dzina lanu mukasiyapo choncho

The Government of Malawi must say no to offshore oil exploitation in Lake Malawi. UK-based Surestream has been contracted for exploration without the mandate of the people. Millions of Malawians however, rely on the lake for food, income, and drinking and cleaning water. Even more take pride in the lake's unparalleled beauty. Malawians know that were oil to be developed in the lake, Note: when signing this petition online on the postal code column,you can just put any five digits of your choice because it wont work when you leave it blank. profits would be shipped abroad and an already poor population would be left stripped of their most precious natural resource. The time has come for the government to say no.

Note: when signing this petition online on the postal code column,you can just put any five digits of your choice because it wont work when you leave it blank.

Letter to
EAD The Government of Malawi (EAD)
Ku Boma la Malawi:
Ndikulemba Kalatayi kuti ndionjezerepo dzina langa pa A Malawi ambiri omwe akusutsana ndi Mfundo yofuna kuyenga mafuta mu Nyaja ya Malawe. Musadikire kampani ya Surestream kuti imalize kufufuza mafutawa; kanani lero! A Malawi sangalore kuluza Phindu,Nsomba ndi madzi abwino omwe amapeza kuchoka mu nyanjayi, komanso a Malawi akudziwa bwino kuti phindu la mafutawa lizangopindulira mabungwe ndi anthu ochepa a chuma kale. Musawalande anthu osauka Nyanja yawo ya mtengo wapatali.
Ine,


----------------
To the Government of Malawi:
I am writing to add my name to the masses of Malawians who oppose offshore oil exploitation in Lake Malawi. Do not wait for Surestream to complete their exploration process; say no today! Malawians cannot afford to lose the income, fish, and clean water they use from the lake, and they know that oil profits would only benefit a few already powerful corporations and individuals. Do not strip an already poor people of their most precious resource.

Sincerely,

Kwame Falo Phiri started this petition with a single signature, and now has 1,257 supporters. Start a petition today to change something you care about.